1 Mbiri 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Davide, Alevi onse onyamula Likasa, oimba, ndi Kenaniya+ mtsogoleri pa ntchito yonyamula katundu imene oimba+ anali kugwira, anavala malaya akunja odula manja, ansalu yabwino kwambiri. Koma Davide anavalanso efodi+ wansalu.
27 Davide, Alevi onse onyamula Likasa, oimba, ndi Kenaniya+ mtsogoleri pa ntchito yonyamula katundu imene oimba+ anali kugwira, anavala malaya akunja odula manja, ansalu yabwino kwambiri. Koma Davide anavalanso efodi+ wansalu.