Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mfumuyo inapanga zochirikizira nyumba ya Yehova+ ndi nyumba ya mfumu, pogwiritsira ntchito matabwa a m’bawawo. Inapanganso azeze+ ndi zoimbira za zingwe+ n’kupatsa oimba. Matabwa a m’bawa ochuluka chonchi sanayambe abwerapo kapena kuonedwapo mpaka lero.

  • 1 Mbiri 9:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+

  • 2 Mbiri 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo Alevi+ oimba a m’gulu la Asafu,+ Hemani,+ Yedutuni,+ ana awo ndi abale awo, onsewa atavala zovala zabwino kwambiri atanyamula zinganga,+ zoimbira za zingwe+ ndi azeze,+ anaimirira kum’mawa kwa guwa lansembe pamodzi ndi ansembe okwanira 120 oimba malipenga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena