1 Mbiri 16:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani+ ndi Yedutuni ndiponso amuna onse amene anasankhidwa+ mwa kutchulidwa mayina kuti aziyamika Yehova,+ chifukwa “kukoma mtima kwake kosatha kudzakhala mpaka kalekale.”+ 1 Mbiri 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya,+ Zeri,+ Yesaiya,+ Simeyi, Hasabiya, ndi Matitiya,+ ana 6. Iwowa anali kuyang’aniridwa ndi Yedutuni bambo wawo, amene anali kulosera ndi zeze poyamika ndi potamanda Yehova.+
41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani+ ndi Yedutuni ndiponso amuna onse amene anasankhidwa+ mwa kutchulidwa mayina kuti aziyamika Yehova,+ chifukwa “kukoma mtima kwake kosatha kudzakhala mpaka kalekale.”+
3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya,+ Zeri,+ Yesaiya,+ Simeyi, Hasabiya, ndi Matitiya,+ ana 6. Iwowa anali kuyang’aniridwa ndi Yedutuni bambo wawo, amene anali kulosera ndi zeze poyamika ndi potamanda Yehova.+