1 Mbiri 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 M’bale wake Asafu+ anali kutumikira mbali ya kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya,+ Berekiya anali mwana wa Simeya, 1 Mbiri 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalinso oimba awa: Hemani,+ Asafu,+ ndi Etani, kuti aimbe zinganga zamkuwa mokweza.+
39 M’bale wake Asafu+ anali kutumikira mbali ya kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya,+ Berekiya anali mwana wa Simeya,