Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Davide ndi atsogoleri+ a magulu a anthu otumikira,+ anapatula ena mwa ana a Asafu, a Hemani,+ ndi a Yedutuni,+ kuti azitumikira. Amuna atatuwa anali kulosera ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ ndi zinganga.+ Mwa ana awo anatengamo amuna ena n’kuwaika pa udindo kuti azitumikira.

  • 2 Mbiri 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo Alevi+ oimba a m’gulu la Asafu,+ Hemani,+ Yedutuni,+ ana awo ndi abale awo, onsewa atavala zovala zabwino kwambiri atanyamula zinganga,+ zoimbira za zingwe+ ndi azeze,+ anaimirira kum’mawa kwa guwa lansembe pamodzi ndi ansembe okwanira 120 oimba malipenga.+

  • 2 Mbiri 29:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Tsopano mfumu Hezekiya ndi akalonga+ anauza Alevi kuti atamande Yehova ndi mawu a Davide+ ndi a wamasomphenya Asafu.+ Chotero iwo anayamba kutamanda Mulungu mosangalala+ ndipo anakhalabe chogwada atawerama mpaka mphumi zawo pansi.+

  • Salimo 50:kam
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • Nyimbo ya Asafu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena