2 Mbiri 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumuyo inapanga masitepe a nyumba ya Yehova ndi a nyumba ya mfumu+ pogwiritsira ntchito matabwa a m’bawawo.+ Inapanganso azeze+ ndi zoimbira za zingwe+ n’kupatsa oimba.+ Zinthu zamtundu umenewu zinali zisanaonekepo m’dziko la Yuda.
11 Mfumuyo inapanga masitepe a nyumba ya Yehova ndi a nyumba ya mfumu+ pogwiritsira ntchito matabwa a m’bawawo.+ Inapanganso azeze+ ndi zoimbira za zingwe+ n’kupatsa oimba.+ Zinthu zamtundu umenewu zinali zisanaonekepo m’dziko la Yuda.