Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 6:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Awa ndiwo anali kutumikira, komanso ana awo: Pa ana a Akohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,+

  • 1 Mbiri 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero Alevi anatenga Hemani+ mwana wa Yoweli n’kumuika pamalo ake. Kenako, pa abale ake, anatengapo Asafu+ mwana wa Berekiya n’kumuika pamalo ake. Pa abale awo, ana a Merari, anatengapo Etani+ mwana wa Kusaya n’kumuika pamalo ake.

  • 1 Mbiri 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ana onsewa anali kuyang’aniridwa ndi bambo awo poimba nyimbo m’nyumba ya Yehova. Ankaimba nyimbozo ndi zinganga,+ zoimbira za zingwe,+ ndi azeze,+ pochita utumiki wa panyumba ya Mulungu woona.

      Koma Asafu, Yedutuni, ndi Hemani anali kuyang’aniridwa ndi mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena