1 Mbiri 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pa ana a Merari,+ abale awo amene anali kumanzere kwawo, panali Etani+ mwana wa Kisa.+ Kisa anali mwana wa Abidi, Abidi anali mwana wa Maluki,
44 Pa ana a Merari,+ abale awo amene anali kumanzere kwawo, panali Etani+ mwana wa Kisa.+ Kisa anali mwana wa Abidi, Abidi anali mwana wa Maluki,