1 Mbiri 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalinso oimba awa: Hemani,+ Asafu,+ ndi Etani, kuti aimbe zinganga zamkuwa mokweza.+