1 Mbiri 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Awa ndiwo anali kutumikira, komanso ana awo: Pa ana a Akohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,+ 1 Mbiri 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onsewa anali ana a Hemani, wamasomphenya+ wa mfumu pa zinthu za Mulungu woona komanso wokweza nyanga* yake pofuna kutamanda Mulungu. Choncho Mulungu woona anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.+
33 Awa ndiwo anali kutumikira, komanso ana awo: Pa ana a Akohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,+
5 Onsewa anali ana a Hemani, wamasomphenya+ wa mfumu pa zinthu za Mulungu woona komanso wokweza nyanga* yake pofuna kutamanda Mulungu. Choncho Mulungu woona anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.+