1 Samueli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wake woyamba dzina lake anali Yoweli,+ ndipo mwana wake wachiwiri anali Abiya.+ Amenewa anali oweruza ku Beere-seba. 1 Mbiri 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana a Samueli+ anali awa: woyamba Yoweli, wachiwiri Abiya.+
2 Mwana wake woyamba dzina lake anali Yoweli,+ ndipo mwana wake wachiwiri anali Abiya.+ Amenewa anali oweruza ku Beere-seba.