1 Mbiri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chiwerengero chawo, pamodzi ndi abale awo ophunzitsidwa kuimbira Yehova,+ onse akatswiri,+ chinakwana 288. Miyambo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kodi wamuona munthu waluso pa ntchito yake? Iye adzaima pamaso pa mafumu.+ Sadzaima pamaso pa anthu wamba.
7 Chiwerengero chawo, pamodzi ndi abale awo ophunzitsidwa kuimbira Yehova,+ onse akatswiri,+ chinakwana 288.
29 Kodi wamuona munthu waluso pa ntchito yake? Iye adzaima pamaso pa mafumu.+ Sadzaima pamaso pa anthu wamba.