2 Mbiri 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno iwo anayamba kukhalamo ndipo anakumangirani malo opatulika a dzina lanu m’dzikolo,+ n’kunena kuti, Salimo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Liwu la Yehova likuchititsa mbawala zazikazi kuphiriphitha ndi ululu wa pobereka,+Ndipo likufafaniza nkhalango.+M’kachisi wake aliyense akunena kuti: “Ulemerero ndi wa Mulungu!”+ Salimo 116:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’mabwalo a nyumba ya Yehova,+Pakati pa iwe Yerusalemu.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Salimo 134:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene mukupemphera mutakweza manja anu, muzikhala oyera,+Ndipo tamandani Yehova.+
8 Ndiyeno iwo anayamba kukhalamo ndipo anakumangirani malo opatulika a dzina lanu m’dzikolo,+ n’kunena kuti,
9 Liwu la Yehova likuchititsa mbawala zazikazi kuphiriphitha ndi ululu wa pobereka,+Ndipo likufafaniza nkhalango.+M’kachisi wake aliyense akunena kuti: “Ulemerero ndi wa Mulungu!”+