Salimo 48:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, ife talingalira mozama za kukoma mtima kwanu kosatha,+Tili mkati mwa kachisi wanu.+ Salimo 63:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho ndakuonani m’malo oyera,+Chifukwa ndaona mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.+ Salimo 134:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 134 Tamandani Yehova,+Inu nonse atumiki a Yehova,+Inu amene mumaimirira m’nyumba ya Yehova usiku.+ Salimo 135:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu amene mukuimirira m’nyumba ya Yehova,+M’mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.+