Salimo 77:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Mulungu, njira yanu ili m’malo oyera.+Kodi ndi Mulungu wamkulu uti amene angafanane ndi Mulungu wathu?+
13 Inu Mulungu, njira yanu ili m’malo oyera.+Kodi ndi Mulungu wamkulu uti amene angafanane ndi Mulungu wathu?+