Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 89:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Mulungu wa makamu,+Ndani ali ndi mphamvu ngati inu Ya?+Ndinu wokhulupirika pa chilichonse.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
8 Inu Yehova Mulungu wa makamu,+Ndani ali ndi mphamvu ngati inu Ya?+Ndinu wokhulupirika pa chilichonse.+