Ekisodo 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Farao sadzakumverani inu.+ Izi zili choncho kuti ndichite zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.”+
9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Farao sadzakumverani inu.+ Izi zili choncho kuti ndichite zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.”+