Ekisodo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+ Yeremiya 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munachita zizindikiro ndi zozizwitsa m’dziko la Iguputo. Zimene munachitazo zikudziwikabe mpaka pano mu Isiraeli ndiponso pakati pa anthu onse.+ Munachita zimenezo kuti mudzipangire dzina mofanana ndi zimene mukufuna kuchita posachedwapa.+
3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+
20 Inu munachita zizindikiro ndi zozizwitsa m’dziko la Iguputo. Zimene munachitazo zikudziwikabe mpaka pano mu Isiraeli ndiponso pakati pa anthu onse.+ Munachita zimenezo kuti mudzipangire dzina mofanana ndi zimene mukufuna kuchita posachedwapa.+