Ekisodo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+ Ekisodo 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Farao sadzakumverani inu.+ Izi zili choncho kuti ndichite zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.”+ Salimo 105:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwowa anasonyeza Aiguputo zizindikiro za Mulungu,+Ndi zozizwitsa m’dziko la Hamu.+ Machitidwe 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+
20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+
9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Farao sadzakumverani inu.+ Izi zili choncho kuti ndichite zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.”+
36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+