Ekisodo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ine ndikudziwa bwino kuti mfumu ya Iguputo sidzakulolani kupita kufikira nditaisonyeza mphamvu zanga.+ Ekisodo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+ Aroma 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+
19 Koma ine ndikudziwa bwino kuti mfumu ya Iguputo sidzakulolani kupita kufikira nditaisonyeza mphamvu zanga.+
4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+
18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+