Ekisodo 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chotero Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti ana a Isiraeli apite, monga momwedi Yehova ananenera kudzera mwa Mose.+
35 Chotero Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti ana a Isiraeli apite, monga momwedi Yehova ananenera kudzera mwa Mose.+