Ekisodo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+ Ekisodo 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Aiguputo anaumiriza anthuwo kuti achoke m’dzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+ Deuteronomo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Motero Yehova anali kuchita zizindikiro ndi zozizwitsa+ zazikulu ndiponso zodzetsa masoka, mu Iguputo yense, kwa Farao ndi kwa onse a m’nyumba mwake ife tikuona.+ Salimo 135:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anasonyeza zizindikiro ndi kuchita zozizwitsa pakati pako Iguputo iwe,+Anachita zimenezo kwa Farao ndi kwa atumiki ake onse.+ Machitidwe 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+
3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+
33 Choncho Aiguputo anaumiriza anthuwo kuti achoke m’dzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+
22 Motero Yehova anali kuchita zizindikiro ndi zozizwitsa+ zazikulu ndiponso zodzetsa masoka, mu Iguputo yense, kwa Farao ndi kwa onse a m’nyumba mwake ife tikuona.+
9 Anasonyeza zizindikiro ndi kuchita zozizwitsa pakati pako Iguputo iwe,+Anachita zimenezo kwa Farao ndi kwa atumiki ake onse.+ Machitidwe 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+
36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+