Genesis 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+ Ekisodo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo atumiki a Farao anamuuza kuti: “Kodi munthu uyu akhala ngati msampha kwa ife kufikira liti?+ Lolani anthuwa apite kuti akatumikire Yehova Mulungu wawo. Kodi simukudziwabe kuti Iguputo wawonongeka?”+ Numeri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ana a Isiraeli anayamba kuuza Mose kuti: “Tsopano ife tifa ndithu! Ndithudi titha ife! Tonse titha basi.+
3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+
7 Pamenepo atumiki a Farao anamuuza kuti: “Kodi munthu uyu akhala ngati msampha kwa ife kufikira liti?+ Lolani anthuwa apite kuti akatumikire Yehova Mulungu wawo. Kodi simukudziwabe kuti Iguputo wawonongeka?”+
12 Tsopano ana a Isiraeli anayamba kuuza Mose kuti: “Tsopano ife tifa ndithu! Ndithudi titha ife! Tonse titha basi.+