Genesis 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno, Yehova anagwetsera Farao ndi banja lake miliri yoopsa+ chifukwa cha Sarai, mkazi wa Abulamu.+ Salimo 105:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu sanalole kuti munthu aliyense awachitire zachinyengo,+Koma anadzudzula mafumu chifukwa cha iwo.+
17 Ndiyeno, Yehova anagwetsera Farao ndi banja lake miliri yoopsa+ chifukwa cha Sarai, mkazi wa Abulamu.+
14 Mulungu sanalole kuti munthu aliyense awachitire zachinyengo,+Koma anadzudzula mafumu chifukwa cha iwo.+