Genesis 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Abulamu ndi Nahori anakwatira. Mkazi wa Abulamu anali Sarai,+ pamene mkazi wa Nahori anali Milika,+ mwana wa Harana. Harana ameneyu analinso bambo ake a Yisika. Genesis 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Sarai mkazi wako usamutchulenso kuti Sarai, chifukwa tsopano dzina lake ndi Sara.+ Genesis 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zitatero, Abulahamu anaika Sara mkazi wake m’manda kuphanga la Makipela, moyang’anizana ndi Mamure, kapena kuti Heburoni, m’dziko la Kanani.+
29 Abulamu ndi Nahori anakwatira. Mkazi wa Abulamu anali Sarai,+ pamene mkazi wa Nahori anali Milika,+ mwana wa Harana. Harana ameneyu analinso bambo ake a Yisika.
15 Ndiyeno Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Sarai mkazi wako usamutchulenso kuti Sarai, chifukwa tsopano dzina lake ndi Sara.+
19 Zitatero, Abulahamu anaika Sara mkazi wake m’manda kuphanga la Makipela, moyang’anizana ndi Mamure, kapena kuti Heburoni, m’dziko la Kanani.+