Genesis 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ali pafupi kulowa mu Iguputo, anauza mkazi wake Sarai kuti: “Ndikudziwa ndithu kuti ndiwe mkazi wokongola m’maonekedwe ako.+ Genesis 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Sarai mkazi wako usamutchulenso kuti Sarai, chifukwa tsopano dzina lake ndi Sara.+ Genesis 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe, ndi mlongo wangadi ameneyu. Bambo athu ndi amodzi, tinangosiyana mayi, ndipo ndinam’kwatira.+ 1 Petulo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 monga mmene Sara analili womvera kwa Abulahamu, ndipo anali kumutcha kuti “mbuyanga.”+ Tsopano inuyo mwakhala ana ake, ndipo mukhalabe ana ake mukapitiriza kuchita zabwino ndi kusaopa chochititsa mantha chilichonse.+
11 Ali pafupi kulowa mu Iguputo, anauza mkazi wake Sarai kuti: “Ndikudziwa ndithu kuti ndiwe mkazi wokongola m’maonekedwe ako.+
15 Ndiyeno Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Sarai mkazi wako usamutchulenso kuti Sarai, chifukwa tsopano dzina lake ndi Sara.+
12 Komabe, ndi mlongo wangadi ameneyu. Bambo athu ndi amodzi, tinangosiyana mayi, ndipo ndinam’kwatira.+
6 monga mmene Sara analili womvera kwa Abulahamu, ndipo anali kumutcha kuti “mbuyanga.”+ Tsopano inuyo mwakhala ana ake, ndipo mukhalabe ana ake mukapitiriza kuchita zabwino ndi kusaopa chochititsa mantha chilichonse.+