Miyambo 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Sudzaopa zoopsa zilizonse zadzidzidzi,+ kapena mphepo yamkuntho yowomba oipa, chifukwa ikubwera.+ Afilipi 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Komanso simukuchita mantha m’njira iliyonse ndi okutsutsani.+ Kwa iwo, chimenechi ndi chizindikiro chakuti adzawonongedwa, koma kwa inu, ndi chizindikiro cha chipulumutso.+ Chizindikiro chimenechi n’chochokera kwa Mulungu.
28 Komanso simukuchita mantha m’njira iliyonse ndi okutsutsani.+ Kwa iwo, chimenechi ndi chizindikiro chakuti adzawonongedwa, koma kwa inu, ndi chizindikiro cha chipulumutso.+ Chizindikiro chimenechi n’chochokera kwa Mulungu.