Luka 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati inu mudzapirire, mudzapeza moyo.+ 2 Atesalonika 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Umenewu ndi umboni wakuti Mulungu amaweruza molungama,+ ndipo chifukwa cha zimenezi mwaonedwa kuti ndinu oyenerera ufumu wa Mulungu,+ umene mukuuvutikira.+
5 Umenewu ndi umboni wakuti Mulungu amaweruza molungama,+ ndipo chifukwa cha zimenezi mwaonedwa kuti ndinu oyenerera ufumu wa Mulungu,+ umene mukuuvutikira.+