2 Mbiri 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma inuyo khalani olimba mtima+ ndipo musagwe ulesi,+ pakuti mudzapeza mphoto chifukwa cha ntchito yanu.”+ Aroma 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Si zokhazo, koma tiyeni tikondwere pamene tili m’masautso,+ popeza tikudziwa kuti chisautso chimabala chipiriro.+ Aheberi 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+ 2 Petulo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pa kudziwa zinthu kudziletsa, pa kudziletsa+ kupirira, pa kupirira kudzipereka kwa Mulungu,+
7 Koma inuyo khalani olimba mtima+ ndipo musagwe ulesi,+ pakuti mudzapeza mphoto chifukwa cha ntchito yanu.”+
3 Si zokhazo, koma tiyeni tikondwere pamene tili m’masautso,+ popeza tikudziwa kuti chisautso chimabala chipiriro.+
36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+