Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+ Akolose 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 chifukwa mukudziwa kuti mudzalandira cholowa+ kuchokera kwa Yehova+ monga mphoto yanu. Tumikirani Ambuye wanu, Khristu, monga akapolo.+ Aheberi 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+
12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+
24 chifukwa mukudziwa kuti mudzalandira cholowa+ kuchokera kwa Yehova+ monga mphoto yanu. Tumikirani Ambuye wanu, Khristu, monga akapolo.+
6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+