Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chotero pamene anali kuphunzitsa m’kachisimo Yesu anafuula kuti: “Inu mukundidziwa ine komanso mukudziwa kumene ndikuchokera.+ Ndipo ine sindinabwere mwa kufuna kwanga,+ alipo ndithu amene anandituma,+ koma inu simukumudziwa.+

  • Aroma 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Komabe, kodi angaitane bwanji munthu amene samukhulupirira?+ Angakhulupirire bwanji munthu amene sanamvepo za iye? Angamve bwanji za iye popanda wina kulalikira?+

  • Aheberi 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti Khristu sanalowe m’malo oyera amkatikati opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Tsopano ali kumwamba kuti aonekere pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena