Aheberi 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kumene Yesu, yemwe ndi kalambulabwalo anakalowa chifukwa cha ife.+ Iyeyu wakhala mkulu wa ansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+ Aheberi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye analowa m’malo oyera amkatikati ndi magazi+ ake, osati ndi magazi a mbuzi kapena a ng’ombe zazing’ono zamphongo. Analowa kamodzi kokha m’malo oyera amkatikatiwo, ndipo anatilanditsa kwamuyaya.+ Aheberi 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu.
20 kumene Yesu, yemwe ndi kalambulabwalo anakalowa chifukwa cha ife.+ Iyeyu wakhala mkulu wa ansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+
12 Choncho iye analowa m’malo oyera amkatikati ndi magazi+ ake, osati ndi magazi a mbuzi kapena a ng’ombe zazing’ono zamphongo. Analowa kamodzi kokha m’malo oyera amkatikatiwo, ndipo anatilanditsa kwamuyaya.+
19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu.