Aheberi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye analowa mʼmalo oyera ndi magazi ake,+ osati ndi magazi a mbuzi kapena a ngʼombe zazingʼono zamphongo. Analowa kamodzi kokha mʼmalo oyerawo ndipo anatipulumutsa kwamuyaya.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 183-184 Nsanja ya Olonda,7/1/1998, tsa. 142/15/1991, ptsa. 15-17
12 Iye analowa mʼmalo oyera ndi magazi ake,+ osati ndi magazi a mbuzi kapena a ngʼombe zazingʼono zamphongo. Analowa kamodzi kokha mʼmalo oyerawo ndipo anatipulumutsa kwamuyaya.+