Aheberi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye analowa m’malo oyera amkatikati ndi magazi+ ake, osati ndi magazi a mbuzi kapena a ng’ombe zazing’ono zamphongo. Analowa kamodzi kokha m’malo oyera amkatikatiwo, ndipo anatilanditsa kwamuyaya.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 183-184 Nsanja ya Olonda,7/1/1998, tsa. 142/15/1991, ptsa. 15-17
12 Choncho iye analowa m’malo oyera amkatikati ndi magazi+ ake, osati ndi magazi a mbuzi kapena a ng’ombe zazing’ono zamphongo. Analowa kamodzi kokha m’malo oyera amkatikatiwo, ndipo anatilanditsa kwamuyaya.+