41 Choncho atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda, ali osangalala+ chifukwa chakuti Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.+
13 Koma muzikondwera+ pamene mukugawana nawo masautso a Khristu,+ kuti mukasangalalenso ndi kukondwera kwambiri pa nthawi imene ulemerero wake udzaonekere.*+