Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kondwerani, dumphani ndi chimwemwe,+ chifukwa mphoto+ yanu ndi yaikulu kumwamba, pakuti umu ndi mmenenso anazunzira aneneri+ amene analipo inu musanakhaleko.

  • Machitidwe 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.

  • Aroma 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Si zokhazo, koma tiyeni tikondwere pamene tili m’masautso,+ popeza tikudziwa kuti chisautso chimabala chipiriro.+

  • 2 Akorinto 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chotero ndimasangalala ndi kufooka, zitonzo, zosowa zanga, mazunzo ndi zovuta zina, chifukwa cha Khristu. Pakuti pamene ndili wofooka, m’pamene ndimakhala wamphamvu.+

  • Afilipi 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Zili choncho chifukwa inu munapatsidwa mwayi. Osati mwayi wokhulupirira+ Khristu wokha, komanso wovutika+ chifukwa cha iye.

  • Aheberi 10:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Pakuti munasonyeza chifundo kwa amene anali m’ndende, ndipo munalola mokondwa kuti katundu wanu alandidwe,+ podziwa kuti inuyo muli ndi chuma chabwino kuposa pamenepo ndiponso chokhalitsa.+

  • 1 Petulo 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma muzikondwera+ pamene mukugawana nawo masautso a Khristu,+ kuti mukasangalalenso ndi kukondwera kwambiri pa nthawi imene ulemerero wake udzaonekere.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena