Aheberi 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Munkachitira chifundo anthu amene anali mʼndende, ndipo munkasangalalabe ngakhale katundu wanu akulandidwa,+ podziwa kuti muli ndi chuma chabwino kwambiri ndiponso chokhalitsa.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:34 Nsanja ya Olonda,8/15/2007, ptsa. 30-311/1/2006, ptsa. 22-235/1/2001, ptsa. 13-14
34 Munkachitira chifundo anthu amene anali mʼndende, ndipo munkasangalalabe ngakhale katundu wanu akulandidwa,+ podziwa kuti muli ndi chuma chabwino kwambiri ndiponso chokhalitsa.+