Luka 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inunso ndikukuuzani kuti: Pezani anzanu pogwiritsa ntchito chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni mʼmalo okhala amuyaya.+
9 Inunso ndikukuuzani kuti: Pezani anzanu pogwiritsa ntchito chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni mʼmalo okhala amuyaya.+