Mateyu 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Mfumu idzauza amene ali kudzanja lake lamanja kuti: ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate wanga. Lowani mu Ufumu umene anakukonzerani kuchokera pachiyambi cha dziko lapansi.* Luka 12:20, 21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako aufuna. Nanga zinthu zimene wasungazi zidzakhala za ndani?’+ 21 Umu ndi mmene zimakhalira ndi munthu amene wadziunjikira chuma, koma si wolemera kwa Mulungu.”+
34 Kenako Mfumu idzauza amene ali kudzanja lake lamanja kuti: ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate wanga. Lowani mu Ufumu umene anakukonzerani kuchokera pachiyambi cha dziko lapansi.*
20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako aufuna. Nanga zinthu zimene wasungazi zidzakhala za ndani?’+ 21 Umu ndi mmene zimakhalira ndi munthu amene wadziunjikira chuma, koma si wolemera kwa Mulungu.”+