Machitidwe 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zitatero atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iwo anali osangalala+ chifukwa Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:41 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 40-41 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 135
41 Zitatero atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iwo anali osangalala+ chifukwa Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.