Machitidwe 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda, ali osangalala+ chifukwa chakuti Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:41 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 40-41 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 135
41 Choncho atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda, ali osangalala+ chifukwa chakuti Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.+