Agalatiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+ Akolose 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 chifukwa mukudziwa kuti mudzalandira cholowa+ kuchokera kwa Yehova+ monga mphoto yanu. Tumikirani Ambuye wanu, Khristu, monga akapolo.+
29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+
24 chifukwa mukudziwa kuti mudzalandira cholowa+ kuchokera kwa Yehova+ monga mphoto yanu. Tumikirani Ambuye wanu, Khristu, monga akapolo.+