Genesis 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Sara anayamba kuseka mumtima mwake+ kwinaku akunena kuti: “Kodi mmene ndatheramu, zoona ndingakhaledi ndi chisangalalo chimenechi, komanso ndi mmene mbuyanga wakalambiramu?”+ Aefeso 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe, aliyense wa inu akonde mkazi wake+ ngati mmene amadzikondera yekha, komanso mkazi azilemekeza kwambiri+ mwamuna wake.
12 Chotero Sara anayamba kuseka mumtima mwake+ kwinaku akunena kuti: “Kodi mmene ndatheramu, zoona ndingakhaledi ndi chisangalalo chimenechi, komanso ndi mmene mbuyanga wakalambiramu?”+
33 Komabe, aliyense wa inu akonde mkazi wake+ ngati mmene amadzikondera yekha, komanso mkazi azilemekeza kwambiri+ mwamuna wake.