Luka 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene anali kunena mawu amenewa, mayi wina m’khamu la anthulo anafuula n’kumuuza kuti: “Ndi wodala mayi+ amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!” Aheberi 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+ 1 Petulo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 monga mmene Sara analili womvera kwa Abulahamu, ndipo anali kumutcha kuti “mbuyanga.”+ Tsopano inuyo mwakhala ana ake, ndipo mukhalabe ana ake mukapitiriza kuchita zabwino ndi kusaopa chochititsa mantha chilichonse.+
27 Pamene anali kunena mawu amenewa, mayi wina m’khamu la anthulo anafuula n’kumuuza kuti: “Ndi wodala mayi+ amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”
11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+
6 monga mmene Sara analili womvera kwa Abulahamu, ndipo anali kumutcha kuti “mbuyanga.”+ Tsopano inuyo mwakhala ana ake, ndipo mukhalabe ana ake mukapitiriza kuchita zabwino ndi kusaopa chochititsa mantha chilichonse.+