Luka 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mngelo uja atafika kwa namwaliyu anati: “Mtendere ukhale nawe,+ iwe wodalitsidwa koposawe, Yehova+ ali nawe.”+ Luka 1:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Chifukwa waona malo otsika a kapolo wake.+ Ndipo taonani! kuyambira tsopano mibadwo yonse idzanditcha wodala.+
28 Mngelo uja atafika kwa namwaliyu anati: “Mtendere ukhale nawe,+ iwe wodalitsidwa koposawe, Yehova+ ali nawe.”+
48 Chifukwa waona malo otsika a kapolo wake.+ Ndipo taonani! kuyambira tsopano mibadwo yonse idzanditcha wodala.+