Mateyu 26:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Atafika, Yudasi analunjika kwa Yesu n’kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu Rabi!”+ Ndipo anam’psompsona.+ Maliko 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano anayamba kum’lonjera kuti: “Mtendere ukhale nanu,+ inu Mfumu ya Ayuda!” Yohane 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+
49 Atafika, Yudasi analunjika kwa Yesu n’kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu Rabi!”+ Ndipo anam’psompsona.+
3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+