Genesis 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zimenezi, uthenga unafika kwa Abulahamu wonena kuti: “Panopo Milika+ naye waberekera m’bale wako Nahori+ ana aamuna. Genesis 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma asanamalize kulankhula,+ anangoona Rabeka mwana wa Betuele+ akutuluka mumzindawo. Betuele anali mwana wa Milika,+ ndipo Milika anali mkazi wa Nahori,+ m’bale wake wa Abulahamu. Rabekayo anali atasenza mtsuko paphewa pake.+
20 Pambuyo pa zimenezi, uthenga unafika kwa Abulahamu wonena kuti: “Panopo Milika+ naye waberekera m’bale wako Nahori+ ana aamuna.
15 Koma asanamalize kulankhula,+ anangoona Rabeka mwana wa Betuele+ akutuluka mumzindawo. Betuele anali mwana wa Milika,+ ndipo Milika anali mkazi wa Nahori,+ m’bale wake wa Abulahamu. Rabekayo anali atasenza mtsuko paphewa pake.+