Genesis 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zimenezi, uthenga unafika kwa Abulahamu wonena kuti: “Nayenso Milika waberekera mchimwene wako Nahori ana aamuna.+
20 Pambuyo pa zimenezi, uthenga unafika kwa Abulahamu wonena kuti: “Nayenso Milika waberekera mchimwene wako Nahori ana aamuna.+