34 Kapena kodi Mulungu anayamba wapitapo kukadzitengera mtundu wa anthu pakati pa mtundu wina ndi mayesero,+ zizindikiro,+ zozizwitsa,+ nkhondo,+ dzanja lamphamvu,+ mkono wotambasula,+ ndi zoopsa zazikulu+ zofanana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona?