Ekisodo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+ Ekisodo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Udzakana kundigonjera kufikira liti?+ Lola anthu anga apite kuti akanditumikire. Ekisodo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano ndadziwa kuti Yehova ndiye wamkulu kuposa milungu ina yonse.+ Zimenezi zinaoneka Aiguputo atasonyeza kudzikuza pamaso pa Aisiraeli.”
2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+
3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Udzakana kundigonjera kufikira liti?+ Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.
11 Tsopano ndadziwa kuti Yehova ndiye wamkulu kuposa milungu ina yonse.+ Zimenezi zinaoneka Aiguputo atasonyeza kudzikuza pamaso pa Aisiraeli.”